(CHIDWI CHOMWE MAULAMA A M’DZIKO LA CHIFUMU LA SAUDI ARABIA ALINACHO PA AKUBANJA KWA MTUMIKI NDI MASWAHABA)

MAFUNSO A MPIKISANO WAUKULU WA NO. 13 WA CHAKA CHA 1442 A.H.

عربي English Português Kiswahili Français Chichewa Hausa Amharic
عربي English Português Kiswahili Français Chichewa Hausa Amharic

:MALANGIZO A MPIKISANO

NDIKOLETSEDWA KUPEREKA MAYANKHO OPOSA AMODZI KUCHOKERA KWA WOPIKISANA MMODZI, NDIPO AKAPEDZEKA ADZACHOTSEDWA ONSE.

ADZAWERENGEDWA KUTI WAKHONZA YEMWE AZAYANKHE MAFUNSO ONSE KUYANKHA KOLONDOLA KUPATULA AWIRI OKHA.

WOPAMBANA AKONZEKE KUYANKHA PAKAMWA MAFUNSO ONSE.

NDIKOFUNIKA KUTI MAYANKHO AYANKHIDWE PA INTERNET KUDZERA PA TSAMBA LA MPIKISANO, NDIPO NGATI ATAYANKHIDWA PA MAPEPALA NDIKOFUNIKA KUTI MAYANKHOWO ALOWETSEDWE PA TSAMBA LA MPIKISANOWU.

TSIKU LOMALIDZA KULANDIRA MAYANKHO KUDZERA PA TSAMBA LA INTERNET NDI: 29/10/1442 A.H POMWE NDI PA 26/6/2021.10


مراجع المسابقة

1ـ سؤال وجواب في أهم المهمات، للشيخ عبدالرحمن بن ناصر السعدي
2ـ التنبيهات اللطيفة فيما احتوت عليه الواسطية من المباحث المنيفة، للشيخ عبدالرحمن بن ناصر السعدي
3ـ فتاوى الشيخ محمد بن إبراهيم
4ـ شرح العقيدة الواسطية من تقريرات سماحة الشيخ محمد بن إبراهيم
5ـ العقيدة الصحيحة وما يضادها، للشيخ عبدالعزيز بن باز
6ـ مجموع مقالات وفتاوى متنوعة، للشيخ عبدالعزيز بن باز
7ـ مجموع فتاوى ورسائل ابن عثيمين
8ـ فتاوى الشيخ صالح الفوزان على موقعه

ULENDO WA HAJJ (PA NTHAWI YOTHEKA KUTERO)
MAFONI AMMANJA
MA COMPUTER AMMANJA (TABLET)
previous arrow
next arrow
Slider

:MPHOTO ZA MPIKISANO

KOMITI YOYANG’ANIRA DAWAH MU AFRIKA IDZACHITITSA MAYERE PAKATI PA OPIKISANA OPAMBANA KU LIKULU LAKE. AMPHUMI 7 OYAMBIRIRA PA KOMITI ILIYONSE (KUDZERA M’MAYERE) ADZAPATSIDWA IMODZI MU MPHOTO IZI:

ZOYENERA KUDZIWA NDIZOTI: CHIWERENGERO CHA OPEZA MPHOTO CHIZACHEPETSEDWA M’DZIKO LILILONSE NGATI OCHITANAO MPIKISANO M’DZIKOMO ATACHEPA

أسئلة المسابقة
س1 "وأتولى أصحاب رسول الله ﷺ ورضي الله عنهم وأذكر محاسنهم, وأترضى عنهم, وأستغفر لهم, وأكف عن مساويهم , وأسكت عما شجر بينهم, وأعتقد فضلهم "
القائل هو:
Q1 “NDIMAWAKONDA MASWAHABA A MTUMIKI WA ALLAH (SWA), NDIMATCHULA ZABWINO ZAO, NDIMAWAFUNIRA ZABWINO, NDIMAWAPEMPHERA CHIKHULULUKO, NDIMASIYA ZOFOOKA ZAO, NDIMAKHALA CHETE PA MIKANGANO YAO KOMANSO NDIMAKHULUPIRIRA ZA UBWINO WAO.” YEMWE ADANENA MAWU AMENEWA NDI:


س2 (ولآلهﷺ على الأمة حق لا يشركهم فيه غيرهم يستحقون من زيادة المحبة والموالاة ما لا يستحق سائر قريش)
القائل هو:
Q2 “AKUBANJA LA MTUMIK (SWA)ALI NDIZOYENERA ZOTI UMMA UZIWACHITIRA, ZOMWE SANGATHANDIZANE NDI ENA, AKUYENERA KUKONDEDWA ZEDI NDI KUPHATANA NAO, ZOMWE SAKUYENERA NAZO AQURAISH ENA.” YEMWE ADANENA MAWU AMENEWA NDI:

س3 قال الشيخ حمد بن معمر رحمه الله : "الصحابة أبر هذه الأمة قلوبا وأعمقها علما وأقلها تكلفا وهم سادات الأمة وكاشفو الغمة فالمسلمون بهديهم يهتدون وعلى مناهجهم يسلكون". يستفاد مما سبق:
Q3 SH. HAMAD IBN MA‘MAR (Allah awachitire chifundo) ADATI: “MASWAHABA NDIANTHU ABWINO ZEDI MITIMA MU UMMA UNO, OZINDIKIRA MWAKUYA, OSAKAKITSA, IWO NDIMABWANA A UMMA, OCHOTSA MDIMA, ASILAMU AKUONGOKA NDI CHIONGOKO CHAO, KOMANSO AKUYENDA PA NJIRA ZAO.” MMAWU AMENEWA TIKUPINDULAMO:

س4 قال رحمه الله في بيان عقيدة أهل السنة والجماعة في الصحابة (ونعتقد أنهم أولى الأمة بكل خصلة حميدة، وأسبقهم إلى كل خير، وأبعدهم من كل شر، وأنهم جميعهم عدول مرضيون) القائل هو:
Q4 ADAYANKHULA … (Allah awachitire chifundo) POLONGOSOLA ZA CHIKHULUPIRIRO CHA AHL SSUNA WALJAMAAPA MASWAHABA: “TIKUKHULUPIRIRA ZOTI IWO NDIAMENE AKUYENERA NDI MBIRI ZIRIZONSE ZABWINO MU UMMA UNO, OTSOGOLA PA ZABWINO ZIRIZONSE, OTALIKIRANA ZEDI NDI ZOIPA ZIRIZONSE, NDIKUTINSO ONSEWO NDIACHILUNGAMO KOMANSO OYANJIDWA.” YEMWE ADAYANKHULA MAWU AMENEWA NDI:

س5 قال الشيخ عبدالرحمن السعدي رحمه الله : فمحبة أهل بيت النبي ﷺ واجبة من وجوه:
Q5 SH. ABDURRAHMAN AS-SA‘D (Allah awachitire chifundo) ADATI: “KUWAKONDA AKUBANJA KWA MNENERI (SWA) NDIKOKAKAMIZIDWA PA ZIFUKWA IZI:

س6 قال الشيخ محمد بن إبراهيم آل الشيخ رحمه الله (يقر أهل السنة والجماعة بما تواتر به النقل عن أمير المؤمنين علي بن أبي طالب رضي الله عنه وغيره من أن خير هذه الأمة بعد نبيها أبوبكر ثم عمر رضي الله عنهما )، فيما سبق دلالة على:
Q6 SH. MUHAMMAD IBN IBRAHIM ᾹL-SHEIKH (Allah awachitire chifundo) ADATI: (ANTHU A AHL SSUNA WAL JAMAA AMAVOMEREZA ZOMWE ZALANDIRIDWA MOCHULUKA KUCHOKERA KWA MTSOGOLERI WA OKHULUPIRIRA ALI (SWA) ZOTI: ABWINO MU UMMA UNO PAMBUYO PA MNENERI WAKE; NDI ABU BAKR KENAKO UMAR). MMAWU OMWE ATSOGOLA MULI UMBONI WOTI:

س7 قال الشيخ محمد بن إبراهيم آل الشيخ رحمه الله (من أصول أهل السنة والجماعة التبرؤ من طريق الروافض الذين يبغضون الصحابة، فإنهم لا يقرون لأصحاب رسول الله ﷺ بقول ولا عمل) ، يتضح مما سبق أن الرافضة :
Q7 SH. MUHAMMAD IBN IBRAHIM ᾹL-SHEIKH (Allah awachitire chifundo) ADATI: “MU NGODYA ZA AHL SSUNA WAL JAMAA KUTALIKIRANA NDI JIRA YA MARAWAFIDH OMWE AMAWADA MASWAHABA, CHIFUKWA IWO SAMAWAVOMERA MASWAHABA A MTUMIKI WA ALLAH (SWA) KUDZERA MMAWU NGAKHALE NTCHITO.” MU ZOMWE ZATSOGOLAZI ZIKUDZIWIKA ZOTI MARAWAFIDH:

س8 قال رحمه الله في بيان عقيدة أهل السنة في التفاضل بين الصحابة رضي الله عنهم (ويعتقدون أن أفضلهم أبو بكر الصديق ثم عمر الفاروق ثم عثمان ذو النورين ثم علي المرتضى رضي الله عنهم وبعدهم بقية العشرة، ثم بقية الصحابة رضي الله عنهم أجمعين(
Q8 ADAYANKHULA …. (Allah awachitire chifundo) POLONGOSOLA ZA CHIKHULUPIRIRO CHA AHLSSUNA WAL JAMAA PA KUSIYANA KWA ULEMERERO PAKATI PA MASWAHABA: “AMAKHULUPIRIRA KUTI WABWINO WAO NDI ABU BAKR AS-SWIDDIIQ, KENAKA UMAR AL-FAARUUQ, KENAKA UTHMAN DHU- ANNUURAIN, KENAKO ALI AL-MURTADHA, NDIPO PAMBUYO PAO PAKUBWERA OTSALIRA MU MASWAHABA KHUMI, KENAKA NDIKUBWERA MASWAHABA ENAO.” MAWU AMENEWA ADANENA NDI:

س9 قال رحمه الله في بيان العقيدة الصحيحة في الصحابة (على رأس المؤمنين من هذه الأمة أصحاب رسول الله ﷺ ، فأهل السنة والجماعة يحبونهم ويوالونهم ويعتقدون أنهم خير الناس بعد الأنبياء؛ لقول النبي ﷺ : خير الناس قرني ثم الذين يلونهم ثم الذين يلونهم). القائل هو:
Q9 ADAYANKHULA …. (Allah awachitire chifundo)POLONGOSOLA ZA CHIKHULUPIRIRO CHOLONDOLA PA MASWAHABA (PATSOGOLO PA OKHULUPIRIRA MU UMMA UNO PALI MASWAHABA A MTUMIKI WA ALLAH (SWA) CHONCHO AHL SSUNA WAL JAMAA AMAWAKONDA, AMAPHATANA NAO NDI KUKHULUPIRIRA ZOTI IWO NDI ANTHU ABWINO ZEDI PAMBUYO PA ANENERI; CHIFUKWA CHA MAWU A MNENERI (SWA)WONENA KUTI: “ANTHU ABWINO NDI MBADO WANGA, KENAKA OMWE AKUTSATIRA PA IWO, KENAKONSO OMWE AKUTSATIRA PA IWO.” AMENE ADAYANKHULA MAWU AMENEWA NDI:

س10 قال سماحة الشيخ عبدالعزيز بن باز رحمه الله (يقال للشيعة: نحن معكم في محبة أهل البيت، ومحبة علي رضي الله عنه وأرضاه، وأنه من خيرة أصحاب رسول الله ﷺ ولكن لسنا معكم في أنه معصوم، ولسنا معكم في أنه الخليفة لرسول الله ﷺ ، بل قبله ثلاثة)، يدل ما سبق على :
Q10 SH. ABDULAZIZ IBN BAZI (Allah awachitire chifundo)ADATI: (ZIMANENEDWA KWA MASHIA: IFE TILINANU LIMODZI POWAKONDA AKUBANJA KWA MTUMIKI (SWA)NDI KUMUKONDA ALI (رضي الله عنهم)NDIKUTI IYE ALI MWA MASWAHABA ABWINO ZEDI A MTUMIKI WA ALLAH (SWA)KOMA SITIRI NANU PA ZOTI IYE NDIOTETEZEDWA (KU KULAKWA), KOMANSO SITIRI NANU PA ZOTI IYE NDI MULOWA MMALO WA MTUMIKI WA ALLAH (SWA)KOMA PATSOGOLO PAKE PALI ATATU) MAWU ATSOGOLAWA AKUSONYEZA:
س11 ألف سماحة الشيخ عبدالعزيز بن باز رحمه الله كتباً كثيرة دلت على سعة علمه ومن أهمها في بيان فضل الآل والأصحاب:
Q11 SH. ABDULAZIZ IBN BAZ (Allah awachitire chifundo) ADALEMBA MABUKU AMBIRI OMWE ADASONYEZA KUCHULUKA KWA MAPHUNZIRO AKE, BUKU LOFUNIKA ZEDI NDILOLONGOSOLA ZA UBWINO WA AKUBANJA NDI MASWAHABA:

س12 استمر الشيخ عبد العزيز بن باز رحمه الله في التدريس لسنوات عديدة لمجموعة من كتب السلف وكان من أشمل الكتب التي تتحدث عن الآل والأصحاب:
Q12 ADAPITIRIZA SH. ABDULAZIZ IBN BAZ (Allah awachitire chifundo) KUPHUNZITSA ZAKA ZAMBIRI MULU WA MABUKU A MAULAMA AKALE, MWA MABUKU OMWE AKUKAMBA KWAMBIRI ZA AKUBANJA NDI MASWAHABA NDI:

س13 وصف الشيخ عبدالعزيز بن باز رحمه الله الفصل الذي عقده ابن تيمية رحمه الله بعنوان (اعتقاد أهل السنة والجماعة في الصحابة والآل)و في كتابه القيم (العقيدة الواسطية) بأنه (من أفضل فصول الكتاب ...)، وفي هذا دلالة على:
Q13 SH. IBN BAZ (Allah awachitire chifundo) ADASIMBA GAWO LOMWE ADALEMBA IBN TAIMIYA NDI MUTU WOTI (CHIKHULUPIRIRO CHA AHL SSUNA WAL JAMAA PA MASWAHABA NDI AKUBANJA) M’BUKU LAKE LAMTENGO WAPATALA (AL-AQIDATUL WASWITWIYYA) KUTI (NDIGAWO LABWINO ZEDI M’BUKUMO). PAMENEPA PALI UMBONI WOTI:

س14 قال الشيخ محمد بن عثيمين رحمه الله: (والصحابة كلهم ثقات، ذوو عدل، تقبل رواية الواحد منهم ...) في كلام الشيخ دلالة على:
Q14 SH. MUHAMMAD IBN UTHAIMIN (Allah awachitire chifundo) ADATI: (MASWAHABA ONSE NDI OKHULUPIRIKA KOMANSO ACHILUNGAMO, KULANDIRA KWAO MAHADISI KUMALOLEDWA NGAKHALE ASAKUDZIWIKA MMENE ADALIRI) MMAWU A SHEIKHEWA MULI UMBONI WOTI:

س15 15 : قال الشيخ محمد بن عثيمين رحمه الله (وأهل السنة والجماعة في آل البيت لا يغلون غلو الروافض، ولا ينصبون العداوة لهم نصب النواصب، ولكنهم وسط بين طرفين) . يدل على ما سبق:
Q15 SH. MUHAMMAD IBN UTHAIMIN (Allah awachitire chifundo) ADATI: (AHL SSUNA WAL JAMAA PA AKUBANJA SAPYOLA MALIRE MONGA ACHITIRA MARAWAFIDH, KOMANSO SAIKA CHIDANI CHOWADA IWO MONGA ACHITIRA MANAWASWIB, KOMA IWO ALI PAKATI PA MAGULU AWIRIWA). MAWU ATSOGOLAWA AKUSONYEZA:

س16 قال الشيخ صالح الفوزان: " المقصود بأهل بيت النبي ﷺ في قوله تعالى:

( إِنَّمَا يُرِيدُ اللَّهُ لِيُذْهِبَ عَنكُمُ الرِّجْسَ أَهْلَ الْبَيْتِ وَيُطَهِّرَكُمْ تَطْهِيرًا (33))

بالدرجة الأولى زوجاته عليهن رضوان الله لأن الآية نزلت بسببهن والخطاب لهنَّ .... ويشمل ذلك قرابته عليه الصلاة والسلام ..." يستفاد مما سبق:
Q16 SH. SWALEH AL-FAUZAN (Allah awachitire chifundo) ADATI: “OMWE AKUNENEDWA KUTI NDIAKUBANJA KWA MNENERI (SWA) MU NDIME IYI: (Ndithu Allah akufuna kukuchotserani uve e, inu a kunyumba (ya Mneneri)! Ndi kuti akuyeretseni ndithu) POYAMBIRIRA NDIAZIKAZI AKE, CHIFUKWA NDIMEYI IDAVUMBULUTSIDWA CHIFUKWA CHA IWO, KOMANSO IWO NDIOMWE AKUYANKHULIDWA… CHONCHO AKUBANJA KWAKE (SWA) MU NDIME IMENEYI WOYAMBIRIRA NDIAZIKAZI AKE, KOMA AKULOWAMONSO ABALE AKE (SWA) KOMA AZIKAZE AKE MU NDIME IMENEYI AKULOWA MOYAMBIRIRA CHIFUKWA IWO NDICHO CHIFUKWA CHOVUMBULUTSIRA). PA ZOMWE ZATSOGOLAZI TIKUPINDULA:

س17 جاء في بيان هيئة كبار العلماء في المملكة العربية السعودية أن عقيدة السلف الصالح أهل السنة والجماعة حب الصحابة وموالاتهم والترضي عنهم والاقتداء بهم وبغض من يبغضهم واعتقاد فضلهم وعدالتهم ونشر فضائلهم والاقتداء بهم، وتوقير آل بيت النبي ﷺ وأزواجه وأمهات المؤمنين رضي الله عنهم أجمعين والقيام بحقوقهم ومحبتهم واعتقاد فضلهم) . يستفاد من بيان كبار العلماء ما يلي:
Q17 MU KULONGOSOLA KWA BUNGWE LA MAULAMA AKULUAKULU A DZIKO LACHIFUMU LA SAUDI ARABIA MWABWERA ZOTI: CHIKHULUPIRIRO CHA ANTHU AKALE, ABWINO, AHL SSUNA WAL JAMAA NDICHOWAKONDA MASWAHABA, NDIKUPHATANA NAO, NDIKUWAPEMPHERA CHIYANJO, KUWATSANZIRA, KUDANA NDI YEMWE AKUWADA, KUKHULUPIRIRA ZA UBWINO WAO, CHILUNGAMO CHAO, KUFALITSA UBWINO WAO, KUWALEMEKEZA AKUBANJA KWA MNENERI (SWA) NDI AZIKAZI AKE, KUDZANSO AMAYI A OKHULUPIRIRA, KUWACHITIRA ZOWAYENERA, KUWAKONDA NDI KUKHULUPIRIRA ZA UBWINO WAO). MU KULONGOSOLA KWA MAULAMA AKULUAKULU TIKUPINDULA:

س18 من جهود علماء المملكة العربية السعودية في العناية بالآل والأصحاب إقامة المؤتمرات، ومنها المؤتمر الذي أقيم في المدينة النبوية عام 1438 الموافق لعام 2017 ، وكان عنوانه:
Q18 MU KULIMBIKIRA KWA MAULAMA A MDZIKO LACHIFUMU LA SAUDI ARABIA POIKIRA CHIDWIPA ZA AKUBANJA NDI MASWAHABA,KUCHITITSA MISONKHANO, MWA IMENEYO; MSONKHANOWOMWE UDACHITIDWA MU MZINDA WAAL- MADINA AN-NABAWIYYA CHAKA CHA 1438 CHOMWE CHIKUFANANA NDI 2017, MUTU WAKE UDALI:

س19 نتيجة لما يتعرض له صحابة رسول الله ﷺ رضي الله عنهم من إساءات، وما ينشر في بعض وسائل الإعلام مما يسيء إليهم رضي الله عنهم ، فقد أكدت هيئة كبار العلماء في المملكة العربية السعودية في دورتها الثامنة والسبعين على الآتي: Q19 POTSATIRA CHIPONGWE CHOMWE MASWAHABA A MTUMIKI WA ALLAH (SWA)NDI KUWAIPITSA KOMWE KUKUDZERA MU NJIRA ZOFALITSIRA MAUTHENGA; BUNGWE LA MAULAMA AKULUAKULU MDZIKO LACHIFUMU LA SAUDI ARABIA MU NKUMANO WAO WA 78 WATSINDIKA PA MFUNDO IZI:

س20 مما يبين عناية علماء المملكة العربية السعودية بالآل والأصحاب:
Q20 ZOMWE ZIKUONETSA KUIKIRA CHIDWI KWA MAULAMA A MDZIKO LACHIFUMU LA SAUDI ARABIA ZA AKUBANJA NDI MASWAHABA:

س21 اهتم علماء المملكة العربية السعودية ببيان حقوق آل النبي ﷺ وأصحابه من خلال:
Q21 MAULAMA A MDZIKO LACHIFUMU LA SAUDI ARABIA ACHIRIMIKA KULONGOSOLA ZA MAUFULU A AKUBANJA KWA MNENERI (SWA)NDIMASWAHABA AKE KUDZERA MU:

س22 لعلماء المملكة دروس كثيرة ودورات متنوعة في نشر منهج أهل السنة والجماعة في الآل والأصحاب من خلال:
Q22 MAULAMA A MDZIKO LACHIFUMU ALI NDI MAPHUNZIRO AMBIRI NDI MASEMINALA OSIYANASIYANA POFALITSA NJIRA YA AHL SSUNNA WAL JAMAA PA AKUBANJA NDI MASWAHABA KUDZERA MU:

س23 من أوجه عناية علماء المملكة العربية السعودية بآل بيت النبي ﷺ وأصحابه الكرام:
Q23 MU NJIRA ZOSONYEZA KUIKIRA CHIDWI MA ULAMA A MDZIKO LACHIFUMU LA SAUDI ARABIA PA AKUBANJA KWA MNENERI (SWA) NDI MASWAHABA AKE OLEMEKEZEKA:

س24 تتجلى عناية علماء المملكة العربية السعودية بآل بيت النبي ﷺ وأصحابه الكرام من خلال حرصهم على:
Q24 KUKUONEKERA KUIKIRA CHIDWI KWA MAULAMA A MDZIKO LACHIFUMU LA SAUDI ARABIA PA AKUBANJA KWA MNENERI (SWA) NDI MASWAHABA AKE OLEMEKEZEKA KUDZERA MU CHIDWI CHAO PA:

س25 تتجلى عناية علماء المملكة العربية السعودية بآل بيت النبي ﷺ وأصحابه الكرام من خلال حرصهم على:
Q25 KUKUONEKERA KUIKIRA CHIDWI KWA MAULAMA A MDZIKO LACHIFUMU LA SAUDI ARABIA PA AKUBANJA KWA MNENERI(SWA) NDI MASWAHABA AKE OLEMEKEZEKA KUDZERA MU CHIDWI CHAO PA:

س26 العناية بفقه الآل والأصحاب أحد أوجه عناية علماء المملكة العربية السعودية بآل بيت النبي ﷺ وصحابته الكرام، ومن ذلك تأليف كتاب )معجم فقه السلف صحابة وعترة وتابعين( الذي جمعه مؤلفه بتكليف من:
Q26 KUIKIRA CHIDWI ZA MAPHUNZIRO A AKUBANJA NDI MASWAHABA NDINJIRA IMODZI YOWONETSA CHIDWI MAULAMA A MDZIKO LACHIFUMU LA SAUDI ARABIA PA AKUBANJA KWA MNENERI(SWA) NDI MASWAHABA OLEMEKEZEKA, MU ZIMENEZO KULEMBA BUKU LA (MU‘UJAM FIQIH AS-SALAF SWAHABATA WA ITRAT WA TAABI‘IN) LOMWE WOLEMBAYO ADALILEMBA MOTUMIDWA NDI:

س27 منهج علماء المملكة العربية السعودية نحو الآل والأصحاب:
Q27 NJIRA YA MAULAMA A MDZIKO LACHIFUMU LA SAUDI ARABIA YOKHUZANA NDI AKUBANJA NDI MASWAHABA:

س28 العناية ببيان الأحكام الفقهية المتعلقة بآل بيت النبي ﷺ من خلال تأليف الكتب أحد أوجه عناية علماء المملكة العربية السعودية بهم رضي الله عنهم ، ومن ذلك كتاب:
Q28 KUIKIRA CHIDWI ZOFOTOKOZA MALAMULO A FIQHI OKHUZANA NDI AKUBANJA KWA MNENERI (SWA) KUDZERA MU KULEMBA MABUKU NDI NJIRA IMODZI YA KUIKIRA CHIDWI KWA MAULAMA A MDZIKO LACHIFUMU LA SAUDI ARABIA ZA IWO, MWA MABUKU AMENEWA NDI:

س29 إبراز مكانة آل بيت النبي ﷺ وبيان فضلهم أحد أبرز اهتمامات علماء المملكة العربية السعودية، ومن ذلك:
Q29 KUSONYEZA ULEMERERO WA AKUBANJA KWA MNENERI (SWA) NDI KULONGOSOLA ZA UBWINO WAO NDICHIMODZI MU ZINTHU ZOONEKERA ZEDI MU ZOMWE MAULAMA A MDZIKO LACHIFUMU LA SAUDI ARABIA AKUIKIRAPO MTIMA, MU ZIMENEZO KULEMBA BUKU LA: amshushie

س30 كتابة الرسائل العلمية للحصول على شهادتي الماجستير والدكتوراه عن الصحابة وآل البيت أحد أوجه عناية علماء المملكة العربية السعودية بهم رضي الله عنهم ومن ذلك:
Q30 KULEMBA MABUKU AMAPHUNZIRO OPEZERA DIGILI YA MASITASI NDI PHD PA ZOKHUZANA NDI MASWAHABA NDI AKUBANJA NDI IMODZI MUNJIRA ZA KUIKIRA CHIDWI KWA MAULAMA A MDZIKO LA CHIFUMU LA SAUDI ARABIA PA ZA IWO, MONGA BUKU LA:

ZOKHUZANA NDI WOPIKISANA:
MWAMUNA MKADZI

ZOMWE KUMAPETO KULI NYENYEZI( * ) ZIYENERA KUPEZEKA NDITHU.


Close Menu